Cânticos 2

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero (NYA)

1 Ine ndine duwa la ku Saroni,

2 Monga duwa lokongola pakati pa minga

3 Monga mtengo wa apulosi pakati pa mitengo ya mʼnkhalango

4 Iye wanditengera ku nyumba yaphwando,

5 Undidyetse keke ya mphesa zowuma,

6 Mutu wanga watsamira dzanja lake lamanzere,

7 Inu akazi a ku Yerusalemu, ndithu ndikukupemphani

8 Tamverani bwenzi langa!

9 Bwenzi langa ali ngati gwape kapena mwana wa mbawala.

10 Bwenzi langa anayankha ndipo anati kwa ine,

11 Ona, nyengo yozizira yatha;

12 Maluwa ayamba kuoneka pa dziko lapansi;

13 Mtengo wankhuyu ukubereka zipatso zake zoyambirira;

14 Nkhunda yanga yokhala mʼmingʼalu ya thanthwe,

15 Mutigwirire nkhandwe,

16 Bwenzi langa ndi wangadi ndipo ine ndine wake;

17 Kamphepo kamadzulo kakayamba kuwuzira

Ler em outra tradução

Comparar lado a lado

Estude este capítulo no WhatsApp

Peça à IA da Bíblia Fala para explicar Cânticos 2, comparar traduções ou montar um estudo — tudo direto pelo WhatsApp.